Baibulo limayankhula za mitundu yambiri ya mwazi: mwazi wa mbuzi, mwazi wa nkhosa, mwazi wa nkhunda! Baibulo limatiuzanso kuti popanda kukhetsa mwazi palibe kukhululukidwa kwa machimo. Ndiye kodi umodzi mwa mitundu iyi ungather kuchotsa machimo?yankho ndi ‘Ayi’ wotsindika. Ndiye ndi chani chingachotse machimo athu? Palibe, koma mwazi wa Yesu Khristu! Ndi mwazi wa Yesu wokhawo umene uli ndi mphamvu kukachotsa machimo athu ndi kutibweretsera chipulumutso.
Mu bukhu lofunikira kwambiri limeri, muzapeza zilungamo zoyera kwambiri zokhuzana ndi mwazi wa Yesu Khristu. Mupeza momwe mwazi wa Yesu umaperekera moyo ndi momwe mwazi wa Yesu unapezera kufunikira kwake. Muzamvetsetsa chiyanjano cha pakati pa Mzimu Woyera ndi mwazi wa Yesu. Mulidi mphamvu mu mwazi wa Yesu!

Mphamvu Ya Mwazi
Mphamvu Ya Mwazi
Product Details
BN ID: | 2940156024322 |
---|---|
Publisher: | Dag Heward-Mills |
Publication date: | 03/22/2019 |
Sold by: | Smashwords |
Format: | eBook |
File size: | 551 KB |
Language: | Undetermined |