Pamene muyenda mmoyo inu mukapeza kuti dziko lobisika ndi dziko lenileni ndipo dziko lakuthupi ndi chiwonetsero cha zina mwa zinthu zamu dziko lobisika. Monga mmene mulili ndi adani owoneka, inu mulinso ndi adani obisika. Kodi mungamenyane ndi mdani osamudziwa iye, ndondomeko zake, kapangidwe kake ka zinthu ndi zida zake? Bukhu ili ndi chida chofunika ku ulendo wa moyo wanu. M'bukhu ili mukaphunzira kuti adani anu obisika ndi ati, mizu yakukhala kwawo, maonekedwe awo ndi momwe mungapambanire nkhondo ndi iwo.
Bukhu labwinoli likuthandizeni kugonjetsa adani anu obisika!

![Dziwani Adani Anu Osawoneka ... ndi kuwagonjetsa!](http://img.images-bn.com/static/redesign/srcs/images/grey-box.png?v11.10.4)
Dziwani Adani Anu Osawoneka ... ndi kuwagonjetsa!

Product Details
BN ID: | 2940163453467 |
---|---|
Publisher: | Dag Heward-Mills |
Publication date: | 01/26/2020 |
Sold by: | Smashwords |
Format: | eBook |
File size: | 3 MB |
Language: | Nyanja |